Hebrews 7:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nkhaniyi imamveka bwino koposa pamene tiwona kuti pafika wansembe wina wonga Melkizedeki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kwadziwikatu koposa ndithu, ngati auka wansembe wina monga mwa mafanidwe a Melkizedeki,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo zimene tanenazi zimamveka bwino ngati tiona kuti pafika wansembe wina wofanana ndi Melikizedeki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kwadziwikatu koposa ndithu, ngati auka wansembe wina monga mwa mafanidwe a Melikizedeke,