Hebrews 7:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja mau a Mulungu pomuchitira umboni akuti, “Ndiwe wansembe mpaka muyaya, unsembe wake wonga uja wa Melkizedeki.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti amchitira umboni, Iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha monga mwa dongosolo la Melkizedeki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Mulungu anamuchitira umboni kuti, “Iwe ndi wansembe wamuyaya, monga mwa dongosolo la unsembe wa Melikizedeki.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti amcitira umboni, Iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha Monga mwa dongosolo la Melikizedeke.