Hebrews 7:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yesu adaloŵa unsembe wake ndi lumbiro, pamene Mulungu adamuuza kuti, “Ambuye adalumbira, ndipo sadzasintha maganizo ake akuti, ndiwe wansembe mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma Iye ndi lumbiro mwa Iye amene anenana kwa Iye, Walumbira Ambuye ndipo sadzalapa, iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha).
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yesu ankakhala wansembe ndi lumbiro pamene Mulungu anati, “Ambuye analumbira ndipo sangasinthe maganizo ake, ‘Iwe ndi wansembe wamuyaya.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
(pakuti iwotu anayesedwa ansembe kopanda lumbiro; koma iye ndi lumbiro mwa iye emeoe ananena kwa iye, Walumbira Ambuye ndipo sadzalapa, Iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha).