Hebrews 7:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yesu ngwamuyaya, motero unsembe wake ngwosasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma Iye chifukwa kuti akhala Iye nthawi yosatha ali nao unsembe wosasinthika,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yesu popeza ndi wamuyaya, unsembe wake ndi wosatha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma iye cifukwa kuti akhala iye nthawi yosatha ali nao unsembe wosasinthika,