Hebrews 7:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kunena za ansembe olandira chachikhumi aja, amene ndi zidzukulu za Levi, iwoŵa ndi anthu otha kufa. Koma kunena za Melkizedeki, Malembo amamchitira umboni kuti ngwamoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pano anthu ofeka alandira limodzi la magawo khumi; koma apo iye, woti adamchitira umboni kuti ali ndi moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ansembe amene amalandira chakhumi amafa, choncho Melikizedeki ndi wamkulu kuwaposa iwo chifukwa Malemba amamuchitira umboni kuti ndi wamoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pano anthu ofeka alandira limodzi la magawo khumi; koma apo iye, woti adamcitira umboni kuti ali ndi moyo.