Hebrews 7:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwenikweni tingathe kunena kuti pamene Abrahamu ankapereka chachikhumi, Levi yemwe, amene amalandira chachikhumi, adaapereka nao chachikhumicho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kuli ngati kunena, mwa Abrahamu Levinso wakulandira limodzilimodzi la magawo khumi adapereka limodzi la magawo khumi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wina angathe kunena kuti Levi, amene amalandira chakhumi, anapereka chakhumicho kudzera mwa Abrahamu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kuli ngati kunena, mwa Abrahamu Levinso wakulandira limodzi limodzi la magawo khumi adapereka limodzi la magawo khumi;