Hebrews 8:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakunena mau oti, “Chipangano chatsopano”. Mulungu akunena kuti chipangano choyamba nchotha ntchito. Paja chinthu chimene chayamba kutha ntchito nkumakalamba, ndiye kuti chili pafupi kuzimirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakunena Iye, Latsopano, anagugitsa loyambali. Koma chimene chilinkuguga ndi kusukuluka, chayandikira kukanganuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ponena kuti, pangano “latsopano” Mulungu wapanga pangano loyamba lija kukhala lotha ntchito, ndipo chilichonse chimene chayamba kutha ntchito ndi kukalamba, chili pafupi kuchokeratu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakunena iye, Latsopano, anagugitsa loyambali. Koma cimene cirimkuguga ndi kusukuluka, cayandikira kukanganuka.