Hebrews 8:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chipangano choyamba chija chikadakhala changwiro, sipakadafunikanso china m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti loyamba lija likadakhala lopanda chilema sakadafuna malo a lachiwirilo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati pangano loyamba lija likanakhala langwiro, sipakanafunikanso lina mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti loyamba lija likadakhala lopanda cirema sakadafuna malo a laciwirilo.