Hebrews 9:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati munthu alemba Chipangano chosiyira ena chuma, pafunika kutsimikiza kuti wolemba chipanganocho wamwaliradi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti pamene pali chopangiratu pafunika pafike imfa ya wolemberayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati munthu alemba pangano losiyira ena chuma, pafunika kutsimikiza kuti wolemba panganolo wamwaliradi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti pamene pali copangiratu pafunika pafike imfa ya wolemberayo.