Hebrews 9:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja chipangano chotere chilibe mphamvu, asanamwalire wochilemba. Chimakhala ndi mphamvu pokhapokha wochilembayo atamwalira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti chopangiratu chiona mphamvu atafa mwini wake; popeza chilibe mphamvu konse pokhala wolemberayo ali ndi moyo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa pangano lotere limakhala ndi mphamvu ngati wolembayo wamwalira. Siligwira ntchito pamene wolembayo ali ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti copangiratu ciona mphamvu atafa mwini wace; popeza ciribe mphamvu konse pokhala wolemberayo ali ndi moyo;