Hebrews 9:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adaamanga chihema, ndipo m'chipinda chake choyamba munkakhala choikaponyale, tebulo, ndi mikate yoperekedwa kwa Mulungu. Chipinda chimenechi chinkatchedwa “Malo Opatulika.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti chihema chidakonzeka, choyamba chija, m'menemo munali choikapo nyali, ndi gome, ndi mkate woonekera; paja paitanidwa Malo Opatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu ankamanga chihema. Mʼchipinda choyamba munali choyikapo nyale, tebulo ndi buledi woperekedwa kwa Mulungu. Chipinda chimenechi chinkatchedwa Malo Opatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti cihema cidakonzeka, coyamba cija, m'menemo munali coikapo nyali, ndi gome, ndi mkate woonekera; paja paitanidwa Malo Opatulika,