Hebrews 9:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pochita zimenezi adanenerera mau akuti, “Aŵa ndi magazi otsimikizira Chipangano chimene Mulungu walamula kuti mchisunge.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati, Uwu ndi mwazi wa chipangano Mulungu adakulamulani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anati, “Awa ndi magazi a pangano limene Mulungu wakulamulirani kuti mulisunge.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati, 1 Uwu ndi mwazi wa cipangano Mulungu adakulamulirani.