Hebrews 9:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malinga ndi malongosoledwe ameneŵa, ansembe amaloŵa m'chipinda choyamba chija masiku onse pokagwira ntchito zao za chipembedzo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo izi zitakonzeka kotero, ansembe amalowa m'chihema choyamba kosalekeza, ndi kutsiriza kulambirako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zinthu zonsezi zitakonzedwa, ansembe ankalowamo mʼchipinda choyamba chija nthawi ndi nthawi kumatumikiramo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo izi zitakonzeka kotero, ansembe amalowa m'cihema coyamba kosalekeza, ndi kutsiriza kulambirako;