Hosea 11:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Pamene Israele anali mwana, ndinkamukonda. Mwana wangayo ndidamuitana kuti atuluke ku Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Israele anali mwana, ndinamkonda, ndinaitana mwana wanga ali m'Ejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Israeli ali mwana, ndinamukonda, ndipo ndinayitana mwana wanga kuti atuluke mu Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Israyeli anali mwana, ndinamkonda, ndinaitana mwana wanga ali m'Aigupto.