Hosea 12:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe anthu ankapembedza mafano ku Giliyadi. Ndithu mafano ameneŵa adzaonongedwa. Ankapereka nsembe za nkhunzi ku Giligala, koma maguwa ansembewo ndidzaŵasandutsa miyulu ya miyala m'munda.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi Giliyadi ndiye wopanda pake? Akhala achabe konse; m'Giligala aphera nsembe ya ng'ombe; inde maguwa ao a nsembe akunga miulu yamiyala m'michera ya munda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Giliyadi ndi woyipa? Anthu ake ndi achabechabe! Kodi amapereka nsembe za ngʼombe zazimuna ku Giligala? Maguwa awo ansembe adzakhala ngati milu ya miyala mʼmunda molimidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi Gileadi ndiye wopanda pace? akhala acabe konse; m'Giligala aphera nsembe yang'ombe; inde maguwa ao a nsembe akunga miulu yamiyala m'micera ya munda.