Hosea 12:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adatulutsa Aisraele ku Ejipito kudzera mwa mneneri. Ndipo mwa mneneriyo adaŵasungabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwa mneneri Yehova anakweretsa Israele kuchokera m'Ejipito, ndi mwa mneneri anasungika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anagwiritsa ntchito mneneri kuti atulutse Israeli mu Igupto; kudzera mwa mneneriyo Iye anawasamalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwa mneneri Yehova anakweretsa Israyeli kucokera m'Aigupto, ndi mwa mneneri anasungika.