Hosea 12:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akali m'mimba mwa mai wake, Yakobe adakangana ndi mbale wake, ndipo atakula adalimbana ndi Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mimba anagwira kuchitende cha mkulu wake, ndipo atakula mphamvu analimbana ndi Mulungu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akali mʼmimba mwa amayi ake, Yakobo anagwira chidendene cha mʼbale wake; iye atakula analimbana ndi Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mimba anagwira ku citende ca mkuru wace, ndipo atakula mphamvu analimbana ndi Mulungu;