Hosea 12:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Aisraele ali ngati wamalonda wonyenga amene amagwiritsa ntchito masikelo onama. Amakonda kumeta anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiye Mkanani, m'dzanja lake muli miyeso yonyenga, akonda kusautsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wamalonda amagwiritsa ntchito masikelo achinyengo; iyeyo amakonda kubera anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiye Mkanani, m'dzanja lace muli miyeso yonyenga, akonda kusautsa.