Hosea 12:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aefuremu akunena kuti, ‘Ndithu talemera, takhuphuka zedi, wina sangatiloze chala pa kulemera kumeneku.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Efuremu anati, Zedi ndasanduka wolemera, ndadzionera chuma m'ntchito zonse ndinazigwira; sadzapeza mwa ine mphulupulu yokhala tchimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Efereimu amadzitama ponena kuti, “Ndine wolemera kwambiri; ndili ndi chuma chambiri. Palibe amene angandiloze chala chifukwa cha kulemera kwanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Efraimu anati, Zedi ndasanduka wolemera, ndadzionera cuma m'nchito zonse ndinazigwira; sadzapeza mwa ine mphulupulu yokhala cimo.