Hosea 14:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Aisraele, bwererani kwa Chauta, Mulungu wanu, pakuti mwagwa chifukwa cha machimo anu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Israele, bwerera kunka kwa Yehova Mulungu wako; pakuti wagwa mwa mphulupulu yako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe Israeli bwerera kwa Yehova Mulungu wako. Machimo anu ndi amene akugwetsani!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Israyeli, bwerera kumka kwa Yehova Mulungu wako; pakuti wagwa mwa mphulupulu yako.