Hosea 14:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ziphukira zake zidzatambasukira kutali, adzakhala wokongola ngati mtengo wa olivi, adzakhala wonunkhira ngati mkungudza wa ku Lebanoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nthambi zake zidzatambalala, ndi kukoma kwake kudzanga kwa mtengo wa azitona, ndi fungo lake ngati Lebanoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mphukira zake zidzakula. Kukongola kwake kudzakhala ngati mtengo wa olivi, kununkhira kwake ngati mkungudza wa ku Lebanoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nthambi zace zidzatambalala, ndi kukoma kwace kudzanga kwa mtengo waazitona, ndi pfungo lace ngati Lebano.