Hosea 2:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake abale ako uŵauze kuti, “Ndinu anthu a Chauta”, ndiponso kuti, “Chauta wakukondani”.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nenani kwa abale anu, Anthu anga, ndi kwa alongo anu, Wochitidwa-chifundo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nena kwa abale ako kuti, ‘Ndinu anthu anga,’ kwa alongo ako kuti ‘Ndinu okondedwa anga.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nenani kwa abale anu, Anthu anga, ndi kwa alongo anu, Wocitidwa-cifundo.