Hosea 2:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono tamverani, ndidzamkopa mkaziyo, ndidzapita naye ku chipululu ndi kukamsangalatsa ndi mau achikondi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake taonani, ndidzamkopa ndi kunka naye kuchipululu, ndi kulankhula naye momkonda mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma tsopano ndidzamukopa mkaziyo; ndidzapita naye ku chipululu ndipo ndidzamuyankhula mwachikondi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace taonani, ndidzamkopa ndi kumka naye kucipululu, ndi kulankhula naye momkonda mtima.