Hosea 2:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo pondiitana uzidzati, ‘Amuna anga.’ Suzidzatinso, ‘Baala wanga.’ Ndikutero Ine Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzakhala tsiku lomwelo, ati Yehova, udzanditcha Mwamuna wanga, osanditchanso Baala wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsiku limeneli,” Yehova akuti, “udzandiyitana kuti, ‘Amuna anga;’ sudzandiyitananso kuti, ‘Mbuye wanga.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzakhala tsiku lomwelo, ati Yehova, udzandicha Mwamuna wanga, osandichanso Baala wanga.