Hosea 2:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzamletsa kuti asatchulenso maina a Abaala, Ndithu anthu sadzatchulanso maina aowo popembedza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndidzachotsa maina a Abaala m'kamwa mwake; ndipo silidzakumbukikanso dzina lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzachotsa mayina a Abaala pakamwa pake; sadzatchulanso mayina awo popemphera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndidzacotsa maina a Abaala m'kamwa mwace; ndipo silidzakumbukikanso dzina lao.