Hosea 2:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe Israele, ndidzakutomera kuti ukhale mkazi wanga mpaka muyaya. Ndidzakutomera mwaungwiro, mwachilungamo, mwa chikondi chosasinthika, ndiponso mwachifundo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzakutomera ukhale wanga kosatha, inde ndidzakutomera ukhale wanga m'chilungamo, ndi m'chiweruzo, ndi m'ukoma mtima, ndi m'chifundo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakutomera kuti ukhale mkazi wanga mpaka muyaya; ndidzakutomera mwachilungamo, mwaungwiro, mwachikondi ndi mwachifundo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakutomera ukhale wanga kosatha, inde ndidzakutomera ukhale wanga m'cilungamo, ndi m'ciweruzo, ndi m'ukoma mtima, ndi m'cifundo.