Hosea 2:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Nthaŵi imeneyo ndidzamvera mlengalenga, mvula idzagwa pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzachitika tsiku lomwelo, ndidzavomereza, ati Yehova, ndidzavomereza thambo, ndi ilo lidzavomereza dziko lapansi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsiku limenelo Ine ndidzayankha,” akutero Yehova. “Ndidzayankha mlengalenga pempho lake lofuna mitambo ndipo mvula idzagwa pa dziko lapansi;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzacitika tsiku lomwelo, ndidzabvomereza, ati Yehova, ndidzabvomereza thambo, ndi ilo lidzabvomereza dziko lapansi;