Hosea 2:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nchifukwa chake njira yake ndidzaitseka ndi minga. Ndidzamuzinga ndi khoma, kuti asayendenso m'njira zake zakale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake taonani, ndidzatchinga njira yako ndi minga, ndipo ndidzammangira mpanda, kuti asapeze mabande ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho njira yake ndidzayitseka ndi minga; ndidzamuzinga ndi khoma kotero kuti sadzapezanso njira yotulukira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace taonani, ndidzacinga njira yako ndi minga, ndipo ndidzammangira mpanda, kuti asapeze mabande ace.