Hosea 4:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Vinyo, kaya ndi wakale kaya ndi watsopano, amaononga nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chigololo, ndi vinyo, ndi vinyo watsopano, zichotsa mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ku zachiwerewere, ku vinyo wakale ndi watsopano, zimene zimachotsa nzeru zomvetsa zinthu
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cigololo, ndi vinyo, ndi vinyo watsopano, zicotsa mtima,