Hosea 4:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele ndi okanika ngati anaang'ombe. Kodi Chauta angathe kuŵadyetsa tsopano ngati anaankhosa pa busa lokoma?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Israele wachita kuuma khosi ngati ng'ombe yaikazi yaing'ono youma khosi; tsopano Yehova adzawadyetsa ngati mwanawankhosa kuthengo lalikulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli ndi nkhutukumve, ngosamva ngati ana angʼombe. Kodi Yehova angathe kuwaweta bwanji ngati ana ankhosa pa msipu wabwino?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Israyeli wacita kuuma khosi ngati ng'ombe yaikazi yaing'ono youma khosi; tsopano Yehova adzawadyetsa ngati mwana wa nkhosa ku thengo lalikuru.