Hosea 4:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amati akamwa kwambiri, amangochita zigololo. Amakonda zamanyazi kupambana ulemu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chakumwa chao chasasa, achita uhule kosalekeza; akulu ao akonda manyazi kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale pamene zakumwa zawo zatha, amapitiriza kuchita zachiwerewere; atsogoleri awo amakonda kwambiri njira zawo zochititsa manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cakumwa cao casasa, acita citole kosalekeza; akuru ao akonda manyazi kwambiri.