Hosea 4:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzachotsedwa ngati chinthu chotengedwa ndi mphepo, ndipo adzachititsidwa manyazi chifukwa cha nsembe zao zachikunja.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mphepo yamkulunga m'mapiko ake, ndipo adzachita manyazi chifukwa cha nsembe zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzachotsedwa ndi kamvuluvulu ndipo adzachita manyazi chifukwa cha nsembe zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mphepo yamkulunga m'mapiko ace, ndipo adzacita manyazi cifukwa ca nsembe zao.