Hosea 4:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akulumbira monama, kunena zabodza, kupha, kuba ndi kuchita chigololo. Machimo achita kunyanya, ndipo akungophanaphana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kulumbira, ndi kunama, ndi kupha, ndi kuba, ndi kuchita chigololo; aboola, ndi mwazi ukhudzana nao mwazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muli kutemberera kokha, kunama ndi kupha. Kuba ndi kuchita chigololo; machimo achita kunyanya ndipo akungokhalira kuphana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kulumbira, ndi kunama, ndi kupha, ndi kuba, ndi kucita cigololo; aboola, ndi mwazi ukhudzana nao mwazi.