Hosea 4:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ansembe ankati akamachulukirachulukira, ndi m'menenso ankanyanyira kundichimwira. Ndidzasandutsa ulemu wao kuti ukhale manyazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga anachuluka, momwemo anandichimwira; ndidzasanduliza ulemerero wao ukhale manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ansembe ankati akachuluka iwo ankandichimwiranso kwambiri; iwo anasinthanitsa ulemerero wawo ndi chinthu china chonyansa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga anacuruka, momwemo anandicimwira; ndidzasanduliza ulemerero wao ukhale manyazi.