Hosea 4:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amalemererapo pa kuchimwa kwa anthu anga, ndipo amafunitsitsa kuti anthuwo azichimwirachimwira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adyerera tchimo la anthu anga, nakhumbira chosalungama chao, yense ndi mtima wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amalemererapo pa machimo a anthu anga ndipo amafunitsitsa kuti anthuwo azipitiriza kuchimwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adyerera cimo la anthu anga, nakhumbira cosalungama cao, yense ndi mtima wace.