Hosea 4:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ansembewo ndidzaŵachita zomwe ndidzaŵachite anthu. Ndidzaŵalanga chifukwa cha makhalidwe ao oipa ndi kuŵalipsira pa ntchito zaozo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzakhala monga anthu, momwemo wansembe; ndipo ndidzawalanga chifukwa chanjira zao, ndi kuwabwezera machitidwe ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo zidzakhala motere: zochitikira anthu ena, zidzachitikiranso ansembe. Ndidzawalanga onsewo chifukwa cha njira zawo, ndidzawabwezera chifukwa cha machitidwe awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzakhala monga anthu, momwemo wansembe; ndipo ndidzawalanga cifukwa canjira zao, ndi kuwabwezera macitidwe ao.