Hosea 5:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aefuremu akuŵapondereza, akuŵalanga chifukwa chomvera za ena.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Efuremu azunzika, apsinjika pa mlanduwo; pakuti anafuna mwini wake kutsata lamulolo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Efereimu waponderezedwa, akulangidwa chifukwa chotsatira mafano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Efraimu azunzika, apsinjika pa mlanduwo; pakuti anafuna mwini wace kutsata lamulolo.