Hosea 5:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake ndidzaononga Efuremu, monga momwe njenjete zimaonongera nsalu, ndidzakhala ngati chilonda choola pa anthu a ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndikhala kwa Efuremu ngati njenjete, ndi kwa nyumba ya Yuda ngati chivundi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndili ngati njenjete kwa Efereimu, ngati chinthu chowola kwa anthu a ku Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndikhala kwa Efraimu ngati njenjete, ndi kwa nyumba ya Yuda ngati cibvundi.