Hosea 5:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Opandukawo azama kwambiri m'machimo ao, Ine ndidzaŵalanga onsewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo opandukawo analowadi m'zovunda; koma Ine ndine wakuwadzudzula onsewo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Owukira azama mʼmoyo wakupha, Ine ndidzawalanga onsewo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo opandukawo analowadi m'zobvunda; koma Ine ndine wakuwadzudzula onsewo.