Hosea 5:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ntchito zao zoipa zatseka njira yao yobwerera kwa Mulungu wao, pakuti mtima wa kusakhulupirika uli mwa iwo, ndipo salabadako za Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Machitidwe ao sawalola kubwerera kwa Mulungu wao; pakuti mzimu wa uhule uli m'kati mwao, ndipo sadziwa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ntchito zawo siziwalola kubwerera kwa Mulungu wawo. Mʼmitima mwawo muli mzimu wachiwerewere; Iwo sadziwa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Macitidwe ao sawalola kubwerera kwa Mulungu wao; pakuti mzimu wacitole uli m'kati mwao, ndipo sadziwa Yehova.