Hosea 5:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adachita zosakhulupirika kwa Chauta, motero ana ao nawonso si ake a Mulungu. Tsono chipembedzo chao chachikunja chidzaŵaonongetsa pamodzi ndi minda yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anachita mosakhulupirika pa Yehova, pakuti anabala ana achilendo; mwezi wokhala udzawatha tsopano, pamodzi ndi maiko ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo ndi osakhulupirika kwa Yehova; amabereka ana amʼchigololo ndipo chikondwerero chawo cha mwezi watsopano chidzawawononga pamodzi ndi minda yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anacita mosakhulupirika pa Yehova, pakuti anabala ana acilendo; mwezi wokhala udzawatha tsopano, pamodzi ndi maiko ao.