Hosea 6:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Posachedwa adzatitsitsimutsa. Patangopita masiku aŵiri kapena atatu, adzatiwukitsa kuti tikhale ndi moyo pamaso pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atapita masiku awiri adzatitsitsimutsa, tsiku lachitatu adzatiutsa; ndipo tidzakhala ndi moyo pamaso pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakapita masiku awiri adzatitsitsimutsa; pa tsiku lachitatu Iye adzatiukitsa kuti tikhale ndi moyo pamaso pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atapita masiku awiri adzatitsitsimutsa, tsiku lacitatu adzatiutsa; ndipo tidzakhala ndi moyo pamaso pace.