Hosea 6:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma anthuwo adaphwanya chipangano changa monga adachitira Adamu. Potero, adandichitira zosakhulupirika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwo analakwira chipangano ngati Adamu, m'mene anandichitira monyenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga Adamu, anthuwa aphwanya pangano langa, iwo sanakhulupirike kwa Ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwo analakwira cipangano ngati Adamu, m'mene anandicitira monyenga.