Hosea 6:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Giliyadi ndi mzinda wa anthu ochita zoipa, akungophana basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Giliyadi ndiwo mudzi wa ochita zoipa, wa mapazi a mwazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Giliyadi ndi mzinda wa anthu ochita zoyipa, okhala ndi zizindikiro za kuphana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Gileadi ndiwo mudzi wa ocita zoipa, wa mapazi a mwazi.