Hosea 7:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele kunyada kwao komwe kukuŵatsutsa. Koma pa zonsezi sakubwerera kwa Chauta Mulungu wao, sakumfunafuna konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzikuza kwa Israele kumchitira umboni pamaso pake; koma sanabwerere kunka kwa Yehova Mulungu wao, kapena kumfunafuna mwa ichi chonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunyada kwake Israeli kukumutsutsa, koma pa zonsezi iye sakubwerera kwa Yehova Mulungu wake kapena kumufunafuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzikuza kwa Israyeli kumcitira umboni pamaso pace; koma sanabwerera kumka kwa Yehova Mulungu wao, kapena kumfunafuna mwa ici conse.