Hosea 7:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Aefuremu ali ngati nkhunda yopusa, yopanda nzeru. Amaitana Aejipito, namapita ku Asiriya kukapempha chithandizo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Efuremu ali ngati nkhunda yopusa yopanda nzeru; aitanira kwa Ejipito, amuka kwa Asiriya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Efereimu ali ngati nkhunda yopusa yopanda nzeru. Amayitana Igupto namapita ku Asiriya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Efraimu ali ngati nkhunda yopusa yopanda nzeru; aitanira kwa Aigupto, amuka kwa Asuri.