Hosea 7:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale ndimaŵalera ndi kuŵalimbitsa, komabe amandichita zachiwembu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana ndawalangiza ndi lulimbitsa manja ao, andilingiririra choipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinawaphunzitsa ndikuwalimbitsa, koma amandikonzera chiwembu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana ndawalangiza ndi kulimbitsa manja ao, andilingiririra coipa,