Hosea 7:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma saganiza kuti Ine sindiiŵala ntchito zao zoipa. Zolakwa zao zaŵazinga, ndipo sizichoka m'maso mwanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo sanena m'mtima mwao kuti Ine ndikumbukira zoipa zao zonse; tsopano machitidwe ao awazinga; ali pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma sazindikira kuti Ine ndimakumbukira zoyipa zawo zonse. Azunguliridwa ndi zolakwa zawo; ndipo sizichoka mʼmaso mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo sanena m'mtima mwao kuti Ine ndikumbukila zoipa zao zonse; tsopano macitidwe ao awazinga; ali pamaso panga,