Hosea 7:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku la chikondwerero cha mfumu, nduna zake zimadakwa, mfumu nkuloŵa nawo m'gulu la anthu oipanganirana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku la mfumu yathu akalonga adzidwalitsa ndi kutentha kwa vinyo; iye anatambasula dzanja lake pamodzi ndi oseka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku la chikondwerero cha mfumu yathu akalonga amaledzera ndi vinyo, ndipo amalowa mʼgulu la anthu achipongwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku la mfumu yathu akalonga adzidwalitsa ndi kutentha kwa vinyo; iye anatambasula dzanja lace pamodzi ndi oseka.