Hosea 7:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Aefuremu ali ngati keke yopsa kumodzi, chifukwa amasakanizikana ndi anthu a mitundu ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Efuremu asokonezana nayo mitundu ya anthu; Efuremu ndiye kamtanda ka mkate kosatembenuzidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Efereimu wasakanikirana ndi mitundu ya anthu ena; Efereimu ndi buledi amene wapsa mbali imodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Efraimu asokonezana nayo mitundu ya anthu; Efraimu ndiye kamtanda ka mkate kosatembenuzidwa.